Mawu Amunsi
a Malemba amatiphunzitsa mmene tiyenela kuonela nchito na kupumula. M’nkhani ino, tidzakambilana za Sabata imene Aisiraeli anali kusunga wiki iliyonse. Colinga cokambilana zimenezi ni kutithandiza kupendanso bwino mmene timaonela nchito na kupumula.