Mawu Amunsi
a Anthu ambili amakhulupilila kuti Mulungu aliko, koma sam’dziŵa bwino. Kodi kudziŵa Yehova kumatanthauza ciani? Nanga citsanzo ca Mose na Mfumu Davide citiphunzitsa ciani pa nkhani ya mmene tingakhalile pa ubale wolimba na Yehova? Nkhani ino idzayankha mafunso amenewa.