Mawu Amunsi
a Kodi anthu akaloŵa m’banja afunika kubeleka ana? Ngati asankha kutelo, kodi ayenela kubeleka ana angati? Nanga angawaphunzitse bwanji kukonda Yehova na kum’tumikila? M’nkhani ino, tidzakambilana zitsanzo zamakono zokhudza nkhaniyi komanso mfundo za m’Baibo zimene zidzatithandiza kuyankha mafunso amenewa.