abCidziŵitso: Kuyambila na Kabuku kano ka Msonkhano wa Umoyo na Utumiki, namba ya phunzilo ya wam’sukulu aliyense izikhala m’mabulaketi (). Malangizo amene wam’sukulu afunika kugwililapo nchito azicoka m’kabulosha kakuti Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa(th)