Mawu Amunsi
a Mtumwi Paulo anakumana na mavuto ambili mu umoyo wake. M’nthawi zovuta zimenezo, abale ena anali kumulimbikitsa kwambili. M’nkhani ino, tidzakambilana makhalidwe atatu amene anathandiza abale amenewo kucita bwino kwambili polimbikitsa ena. Tidzakambilananso mmene tingalimbikitsile ena potengela citsanzo cawo.