Mawu Amunsi
a Kodi munakumanapo na mavuto amene anakupangitsani kudziona kuti ndinu wacabe-cabe? Nkhani ino, idzatithandiza kukumbukila kuti Yehova amatikonda kwambili na kutiona kukhala ofunika. Tidzakambilana mfundo zimene zingatithandize kuti tizidziona kukhala ofunika mosasamala kanthu za mavuto amene tikukumana nawo.