Mawu Amunsi
c KUFOTOKOZELA MAWU ENA: Cidindo. Kuika cidindo cotsiliza pa Mkhristu wodzozedwa kumacitika akatsala pang’ono kumwalila ali wokhulupilika, kapena kudzacitika cisautso cacikulu citatsala pang’ono kuyamba.—Aef. 4:30; Chiv. 7:2-4; onani nkhani yakuti “Mafunso Ocokela kwa Oŵelenga” mu Nsanja ya Olonda ya April 2016.