Mawu Amunsi
a Caka cino, Cikumbutso ca imfa ya Khristu cidzacitika pa Ciŵili, pa April 7. Kodi Akhristu amene adzadya mkate na kumwa vinyo pa Cikumbutso, tiyenela kuwaona bwanji? Kodi tiyenela kuda nkhawa tikaona kuti ciŵelengelo ca amene amadya mkate na kumwa vinyo pa Cikumbutso cikukwela? Nkhani ino iyankha mafunso amenewa, ndipo yazikidwa pa nkhani imene inatuluka mu Nsanja ya Mlonda ya January 2016.