Mawu Amunsi
a Gulu la Yehova ni la mtendele. Koma mtendele umenewu ungasokonezeke ngati tilola kaduka kukula mu mtima mwathu. M’nkhani ino, tikambilana zimene zimayambitsa kaduka. Tikambilananso zimene tingacite kuti tithetse khalidwe lowononga limeneli komanso mmene tingalimbikitsile mtendele.