Mawu Amunsi
c MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: Pa miting’i ya akulu, bungwe la akulu lapempha m’bale wacikulile kuti aphunzitseko mkulu wacicepele kutsogoza Phunzilo la Nsanja ya Mlonda. Ngakhale kuti m’bale wacikulileyo amaukonda utumikiwo, iye akugwilizana na cosankha ca akuluwo na mtima wonse. Akupeleka malangizo othandiza kwa m’bale wacicepeleyo na kumuyamikila mocokela pansi pa mtima.