Mawu Amunsi
a Ife tonse nthawi zina timakhala na nkhawa cifukwa ca mavuto amene timakumana nawo. M’nkhani ino, tikambilana zitsanzo zitatu za atumiki a Yehova a m’nthawi yakale amene anavutikapo na nkhawa. Tikambilananso mmene Yehova anatonthozela aliyense wa iwo.