Mawu Amunsi
a Anthu ena amene amakonda Yehova amakayikila ngati ni okonzeka kubatizika kuti akhale Mboni ya Yehova. Ngati umu ni mmene imwe mumamvelela, nkhani ino idzakuthandizani kuganizila zinthu zina zimene mufunika kucita kuti mukabatizike.