Mawu Amunsi
a Ife anthu opanda ungwilo, timathamangila kuweluza ena na kukayikila zolinga zawo. Koma Yehova “amaona mmene mtima ulili.” (1 Sam. 16:7) M’nkhani ino, tikambilana mmene iye anaonetsela cikondi pothandiza Yona, Eliya, Hagara, komanso Loti. Nkhaniyi itithandiza kudziŵa mmene tingatsatilile citsanzo ca Yehova pocita zinthu na abale na alongo athu.