Mawu Amunsi
c MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: Poyamba, woyang’anila kagulu anali kuona kuti mlongo wina m’kagulu kake ni wamisulo komanso wosafuna kugwilizana na ena. Koma pambuyo pake anazindikila kuti mlongoyo ni wamanyazi cabe, ndipo samasuka akakhala ndi anthu osawadziŵa bwino.