Mawu Amunsi
d MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: Pamene mlongo anaona mlongo wina ku Nyumba ya Ufumu, anaganiza kuti ni wosaganizila ena komanso wokwiya-kwiya. Koma atapatula nthawi yoceza naye kuti amudziŵe bwino, anazindikila kuti mlongoyo ni wabwino-bwino.