Mawu Amunsi
a M’nkhani yapita, tinakambilana za mphatso zingapo zooneka zimene Mulungu anatipatsa. M’nkhani ino, tikambilana za cuma cosaoneka kapena kuti mphatso zosaoneka. Tikambilananso mmene tingaonetsele kuyamikila cuma cimeneco. Nkhaniyi itithandizanso kuti tiziyamikila kwambili Yehova Mulungu, Gwelo la cuma cimeneci.