Mawu Amunsi
a Yehova amafuna kuti Akhristu amene analeka kusonkhana na kulalikila abwelela kwa iye. Pali zambili zimene tingacite kuti tithandize ozilala amene amafuna kulabadila ciitano ca Yehova cakuti: “Bwelelani kwa ine.” M’nkhani ino, tikambilana mmene tingawathandizile kubwelela kwa Yehova.