Mawu Amunsi
c Ozilala ena angathandizidwe mwa kuphunzila nawo mitu ina m’buku lakuti Mmene Tingakhalilebe mu Cikondi ca Mulungu, ndipo ena angapindule mwa kuphunzila nawo mitu ina m’buku lakuti Yandikirani kwa Yehova. Ni udindo wa Komiti ya Utumiki ya Mpingo kusankha wofalitsa woyenelela kutsogoza phunzilo limenelo.