Mawu Amunsi
a Kodi ni nkhani yofunika kwambili iti imene ikhudza anthu onse na angelo? N’cifukwa ciani nkhani imeneyo ni yofunika kwambili? Nanga ise tingacite ciani pothandiza kuthetsa nkhani imeneyo? Kudziŵa mayankho pa mafunso amenewa ndi ena okhudzana na nkhaniyo kungatithandize kulimbitsa ubale wathu na Yehova.