Mawu Amunsi
a M’nkhani ino, tikambilana mbali ya pemphelo la Mfumu Davide yopezeka pa Salimo 86:11, 12. Kodi kuopa dzina la Yehova kutanthauza ciani? N’zinthu ziti zimene zimatisonkhezela kuopa dzina lalikulu limeneli? Nanga kuopa Mulungu kungatiteteze bwanji tikayesedwa kuti ticite zoipa?