Mawu Amunsi
c MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: Hava anagonja ku cilakolako coipa. Mosiyana na iye, ise timapewa kuona zithunzi kapena kuŵelenga mameseji yoipa amene angatipangitse kukhala na zilakolako zoipa zimene zingabweletse citonzo pa dzina la Mulungu.