Mawu Amunsi
a Nkhani ino itithandiza kuona kufunika koyamikila ziphunzitso za coonadi ca m’Mawu a Mulungu. Tionanso zimene zingatithandize kukhala otsimikiza kuti zimene timakhulupilila ni coonadi.