Mawu Amunsi
a M’nkhani ino, tikambilana citsanzo ca mtumwi Paulo. Pokambilana zimenezi, tiona kuti ngati ndife odzicepetsa, Yehova amatipatsa mphamvu zotithandiza kupilila pamene tikunyozedwa. Komanso amatipatsa mphamvu pamene tafooka.