Mawu Amunsi
c MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: Pamene Paulo anayamba kulalikila za Khristu, anasiya zinthu zimene anali nazo pamene anali Mfarisi. Mwina zinthu zimenezi zinaphatikizapo mipukutu ya maphunzilo ake akudziko, komanso kaphukusi kokhala na malemba.