Mawu Amunsi
a Kuyembekezela kukwanilitsika kwa malonjezo a Mulungu kungayese kuleza mtima kwathu, ngakhalenso cikhulupililo cathu. Kodi ni mfundo zotani zimene tingaphunzile pa citsanzo ca Abulahamu, zimene zingatithandize kuti tiziyembekezela moleza mtima malonjezo a Yehova? Nanga tingaphunzile ciani pa zitsanzo zabwino za atumiki a Yehova amakono?