Mawu Amunsi
b KUFOTOKOZELA MAWU ENA: Malo amene tili nawo mu mpingo wa Yehova, atanthauza mbali imene timacita polimbikitsa mpingo. Ndipo malo amenewa sadalila mtundu, fuko, cuma, banja, miyambo, kapena maphunzilo amene tili nawo.