Mawu Amunsi
c MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: Zithunzi zitatuzo zionetsa zimene zimacitika msonkhano wa pa mpingo usanayambe, uli mkati, komanso ukatha. Cithunzi coyamba: Mkulu apatsa mlendo moni mwacimwemwe, m’bale wacinyamata akonza zolankhulila, ndiponso mlongo aceza na mlongo wokalamba. Caciŵili: Acikulile na acicepele omwe, akupeleka ndemanga pa Phunzilo la Nsanja ya Mlonda. Cacitatu: Okwatilana athandiza kuyeletsa mu Nyumba ya Ufumu. Mayi athandiza mwana wake kuika copeleka m’bokosi la zopeleka. M’bale wacinyamata asamalila mabuku, komanso m’bale alimbikitsa mlongo wokalamba.