Mawu Amunsi
a Nkhani yapita, inalimbikitsa maphunzilo a Baibo opita patsogolo kulabadila ciitano ca Yesu cakuti akhale asodzi a anthu. Nkhani ino ifotokoza zinthu zitatu zimene ofalitsa onse, kaya atsopano kapena aciyambakale ayenela kucita kuti apitilize kugwila nchito yolalikila za Ufumu mpaka pamene Yehova adzanene kuti yatha.