Mawu Amunsi
a Alongo amakumana na mavuto ambili. M’nkhani ino, tikambilana mmene tingathandizile alongo mumpingo potengela citsanzo ca Yesu. Iye anali kupatula nthawi yoceza na akazi, kuwaonetsa kuti anali ofunika, komanso kuwaikila kumbuyo. Tiona zimene tingaphunzile kwa iye pa mbali zimenezi.