Mawu Amunsi
e MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: Potengela citsanzo ca Yesu cokonda akazi okhulupilika, m’bale akuthandiza alongo aŵili kusintha wilo ku motoka yawo, m’bale wina wapita kukacezela mlongo wodwala, ndipo m’bale winanso na mkazi wake wapita kukacita nawo kulambila kwa pabanja ku nyumba kwa mlongo wina na mwana wake.