Mawu Amunsi
b KUFOTOKOZELA MAWU ENA: Liwu lakuti “mtendele” silitanthauza cabe kusakhalapo kwa nkhondo. Liwu la Ciheberi lomasulidwa kuti mtendele limaphatikizaponso kukhala na umoyo wathanzi, wotetezeka, komanso wosangalala.