Mawu Amunsi
c MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: Mfumu Asa anacotsa ambuye ŵake pa udindo wawo cifukwa anali kulimbikitsa kulambila konama. Anthu amene anali kumbali ya Asa anatengela citsanzo cake mwa kuwononga mafano.