Mawu Amunsi
a Buku lakuti The Finished Mystery inali voliyumu ya namba 7 ya buku lakuti Studies in the Scriptures. Buku la “ZG” la cikuto capepala, linapulintiwa monga Nsanja ya Mlonda ya March 1, 1918. Cilembo ca “Z” cinali kuimila Zion’s Watch Tower, ndipo “G” kuimila cilembo ca namba 7 pa alifabeti, kutanthauza voliyumu ya namba 7.