Mawu Amunsi
a Makolo acikhristu amafuna kuti ana awo akadzakula, akapitilizebe kutumikila Yehova mokondwa. Kodi makolo angapange zosankha zotani kuti athandize ana awo kupitilizabe kutumikila Yehova ngakhale akadzakula? Nanga Akhristu acinyamata afunika kupanga zosankha zotani kuti akakhale na umoyo wopambana kweni-kweni? Nkhani ino iyankha mafunso amenewa.