Mawu Amunsi
a Yesu analamula otsatila ake kupanga ophunzila na kuwaphunzitsa kusunga zinthu zonse zimene iye anawalamula. M’nkhani ino, tiphunzila mmene tingatsatilile malangizo a Yesu. Mfundo zina m’nkhani ino zacokela mu Nsanja ya Olonda ya July 1, 2004, mapeji 14-19.