Mawu Amunsi
a 1 Akorinto caputa 15 imakamba za kuuka kwa akufa. N’cifukwa ciani ciphunzitso cimeneci n’cofunika kwa ife, ndipo tingakhale bwanji otsimikiza kuti Yesu anaukitsidwadi? Nkhani ino iyankha mafunso amenewa komanso ena ofunika kwambili okhudza kuuka kwa akufa.