Mawu Amunsi b MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: Yesu anali woyamba kupita kumwamba. (Mac. 1:9) Ena mwa ophunzila ake amene anali kudzam’tsatila anali Tomasi, Yakobo, Lidiya, Mariya, komanso Paulo.