Mawu Amunsi
c MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: M’bale anataikilidwa mkazi wake wokondeka amene anatumikila naye kwa nthawi yaitali. Iye ali na cikhulupililo cakuti mkazi wake adzaukitsidwa, ndipo akupitiliza kutumikila Yehova mokhulupilika.