Mawu Amunsi
a Mbali yaciŵili ya 1 Akorinto caputa 15, imafotokoza za kuuka kwa akufa, maka-maka kuuka kwa Akhristu odzozedwa. Komabe, zimene mtumwi Paulo analemba zimakhudzanso a nkhosa zina. Nkhani ino itionetsa mmene ciyembekezo cathu cakuti akufa adzauka ciyenela kukhudzila umoyo wathu pali pano, na kutithandiza kuyembekezela za kutsogolo mwacidwi.