Mawu Amunsi
a Yosefe, Naomi na Rute, Mlevi wina wake, komanso mtumwi Petulo anakumana na mavuto olefula. M’nkhani ino, tiona mmene Yehova anawatonthozela na kuwalimbikitsa. Tionenso zimene tingaphunzilepo pa zitsanzo zawo, komanso mmene Mulungu anacitila nawo zinthu mwacifundo.