Mawu Amunsi
d MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: Mlongo amene anali atalefuka kwakanthawi, akukumbukila za utumiki umene anacitapo kumbuyoku, ndipo akupemphela kwa Yehova. Iye akhulupililadi kuti Yehova amadziŵa zimene anacita kumbuyoku komanso zimene akucita palipano.