Mawu Amunsi
b MAWU OFOTOKOZELA ZITHUNZI: Mkulu wacinyamata akulankhula malinga na zimene anaphunzila kwa mkulu wacikulile wacidziŵitso. Ndipo pa cithunzi cina, mkulu wacikulileyo akulandila mkulu wacinyamatayo na mkazi wake amene abwela ku nyumba kwake