Mawu Amunsi
a Mwamuna akakwatila amakhala mutu wa banja latsopano. M’nkhani ino tikambilana zimene umutu umatanthauza, cifukwa cake Yehova anaukhazikitsa, komanso zimene amuna angaphunzile ku citsanzo ca Yehova na Yesu. M’nkhani yotsatila, tidzakambilana zimene mwamuna na mkazi wake angaphunzile kwa Yesu komanso ku zitsanzo zina za m’Baibo. Ndipo nkhani yacitatu idzafotokoza za umutu mu mpingo.