Mawu Amunsi
b Maganizo akuti palibe vuto mwamuna kuvutitsa mkazi wake kapena kum’menya kumene, nthawi zina amaonetsedwa m’mafilimu, m’maseŵelo, komanso m’mabuku a nkhani zoseketsa. Conco, anthu amaona kuti sikulakwa mwamuna kupondeleza mkazi wake.