Mawu Amunsi
a Yehova anakonza zakuti mkazi wokwatiwa azigonjela mwamuna wake. Kodi izi zitanthauza ciani? Amuna na akazi acikhristu angaphunzile zambili pankhani ya kugonjela kucokela kwa Yesu, komanso kwa akazi ena amene nkhani zawo zinalembedwa m’Baibo.