Mawu Amunsi
a Nkhani zambili m’Baibo zimaonetsa kuti Yehova amakonda atumiki ake ndipo adzawathandiza pa mayeso awo onse. Nkhani ino idzafotokoza mmene tingacitile phunzilo la Baibo laumwini limene lingatithandize kupindula kwambili na nkhani zimene tiŵelenga.