Mawu Amunsi
b Njila ya kaphunzilidwe imene taipeleka monga lingalilo pano, ni imodzi mwa njila zina zimene tingaseŵenzetse pophunzila. Malingalilo ena a mophunzilila Baibo mungawapeze mwa kuyang’ana mu Buku Lofufuzila Nkhani la Mboni za Yehova pansi pa mutu wakuti, “Baibo” pa kamutu kakuti “Kuŵelenga na kumvetsetsa Baibo.”