Mawu Amunsi
a Baibo inalonjeza kuti Yehova adzatilimbitsa na kutiteteza ku zinthu zimene zingatiwononge mwauzimu komanso ku zina zimene zingatiwononge kothelatu. Nkhani ino iyankha mafunso aya: N’cifukwa ciani tiyenela kutetezedwa? Kodi Yehova amatiteteza bwanji? Nanga tifunika kucita ciani kuti tipindule na thandizo limene Yehova amapeleka?