Mawu Amunsi
a Pamene abale acinyamata akukula kuuzimu, amafuna kutumikila Yehova m’njila zambili. Kuti iwo ayenelele kukhala atumiki othandiza, amafunika kukhala odalilika mumpingo. Kodi abale acinyamata angacite ciani kuti abale na alongo mumpingo aziwadalila?