Mawu Amunsi
a Monga Akhristu oona, tifunika ‘kutsatila mapazi a Yesu mosamala kwambili.’ Kodi Yesu anatisiyila “mapazi” otani amene tifunika kutsatila? Nkhani ino iyankha funso limeneli. Ifotokozanso cifukwa cake tiyenela kutsatila mapazi ake mosamala kwambili, na mmene tingacitile zimenezi.